top of page
Mau a masiku onse
Buku iri lidzakutsogolerani m’Baibulo ndi zowerenga za tsiku lirilonse ndi mau ofotokozera ndime za m’Baibulo.
​
Tengani buku APA.
Mupangiridwa kulemba mbali zonse ziwiri.
Katekisma wa Heidelberg
Katekisma wa Heidelberg itiphunzitsa mfundo zikulu-zikulu za m'Baibulo.
Tengani Katekisma wa Heidelberg (Chichewa-Cingerezi) APA.
Zitanthauzo za mau ogwiritsidwa nchito m'Cikristu
Tengani mau APA.
bottom of page