top of page
Stephanos Zambia Trust ndi kabungwe koziimira pa kokha ku Petauke (Zambia). Colinga ca Stephanos Zambia Trust ndi kubweretsa anthu pafupi ndi Mau a Mulungu, Baibulo, kuti adziwe Yesu Kristu.
Tero, Stephanos Zambia Trust ilimbikitsa inu kugawana uthenga womwe upezeka m'webusaiti iri.
KUKAMBIRANA
Ngati muli ndi funso, musacedwe kutiuza.
bottom of page