top of page
Kubadwa kwa Yesu.jpg

MAPHUNZIRO A M'BAIBULO

Ngati mufuna maphunziro a m'Baibulo a nthano zina, conde tiuzeni.

Kulengedwa ndi kucimwa koyamba
Genesis 1-3

Malamulo Khumi a Mulungu
Eksodo 19, Eksodo 20, Eksodo 32, Eksodo 32

Davide
1 Samueli 16, 1 Samueli 17, 1 Samueli 19, 1 Samueli 24, 1 Samueli 31
2 Samueli 1, 2 Samueli 2, 2 Samueli 9, 2 Samueli 11, 2 Samueli 12


Elisa
2 Mafumu 4, 2 Mafumu 6

Nehemiya
Nehemiya 1, Nehemiya 2, Nehemiya 4, Nehemiya 6, Nehemiya 13

Estere
Estere 1-9

Danieli
Danieli 1-6

Kubadwa kwa Ambuye Yesu
Luka 1, Luka 2, Mateyu 2

Zodabwitsa zimene Yesu anacita
Yohane 1.35-51, Yohane 2.1-12, Marko 2.1-12, Marko 4.35-41, Marko 5.1-20, Luka 8.41-56, Marko 6.31-44 ndi Marko 10.46-52


Kufa ndi kuuka kwa Ambuye Yesu
Mateyu 26-28, Luka 23 ndi 24, Yohane 18, 20 ndi 21

Kukwera Kumwamba kwa Yesu, kutumidwa kwa Mzimu Woyera ndi zimene zinacitika kucokera pa nthawi iyo
Macitidwe a Atumwi 1, 2, 9, 12 ndi 16

Petro
Macitidwe a Atumwi 3, 4, 5, 8, 9, 10,12

Paulo
Macitidwe a Atumwi 9, 13, 14, 16, 19, 20, 27 ndi 28

bottom of page