Maphunziro a anyamata ndi atsikana
(a zaka 12-17)
Mitu:
1. Colinga ca miyoyo yathu
2. Kuthetsa mabvuto
3. Ubwenzi
4. Kukakamizidwa ndi abwenzi
5. Kusamalira thupi langa ndi cilengedwe
6. Tsogolo langa
Tengani maphunziro APA.
Maphunziro a anyamata ndi atsikana
(a zaka 18-35)
Mitu:
1. Colinga ca miyoyo yathu ndi kupanga maganizo
2. Kukakamizidwa ndi abwenzi
3. Ubwenzi
4. Matupi athu ndiwo mphatso zocokera kwa Mulungu
5. Cikondi ndi ukwati
6. Kupewa mayesero
Tengani maphunziro APA.
Pemphero la Ambuye
Mitu:
1. Atate wathu wa Kumwamba
2. Dzina lanu liyeretsedwe
3. Ufumu wanu udze
4. Kufuna kwanu kucitidwe
5. Mutipatse ife lero cakudya cathu calero
6. Mutikhululukire mangawa athu monga ifenso takhululukira amangawa anthu
7. Musatitengere ife kokatiyesa koma mutipulumutse kwa woipayo
Tengani maphunziro APA.
Imani nji! Cikhulupiriro ca Atumwi
Mitu:
1. Ndikhulupirira Mulungu
2. Atate wamphamvu wa mphamvu zonse, wakulenga za
kumwamba ndi za pansi.
3. Ndikhulupirira Yesu Kristu, Mwana wake wobadwa yekha,
Ambuye wathu
4. Amene anapatsidwa ndi Mzimu Woyera, nabadwa mwa
Mariya namwaliyo, nasautsidwa kwa Pontio Pilato
5. Namwalira, naikidwa m’manda
6. Natsikira kwa akufa. Tsiku lacitatu anaukanso kwa akufa
7. Nakwera Kumwamba, nakhala padzanja lamanja la Mulungu
Atate wa mphamvu zonse, kucokera komweko adzadza
kudzaweruza anthu amoyo ndi akufa.
8. Ndikhulupirira Mzimu Woyera. Ndikhulupirira Mpingo
wopatulika wa Kristu wa kwa anthu onse
9. Ciyanjano ca oyera mtima, kukhululukidwa kwa macimo
10. Kuukanso kwa thupi, ndi moyo wosatha. Amen.
Tengani maphunziro APA.
Mabanja acikristu
(maphunziro a anthu opezeka m’ukwati ndi a makolo)
Mitu:
1. Maziko a ukwati wacikristu
2. Ukwati wacikristu
3. Azimuna acikristu
4. Azimai acikristu
5. Makolo acikristu monga zitsanzo
6. Makolo acikristu monga aziphunzitsi
7. Mabanja acikristu
Tengani maphunziro APA.
Umoyo wacikristu
Mitu:
1. Baibulo
2. Thanzi ndi matenda
3. Cuma ndi umphawi
4. Pemphero
5. Coonadi ndi cinyengo
Tengani maphunziro APA.